Salimo 65:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mumanyowetsa minda yake komanso kusalaza dothi limene lalimidwa,*Mumaifewetsa ndi mvula yamvumbi. Mumadalitsa zomera zake.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:10 Chisungiko cha Padziko Lonse, tsa. 175
10 Mumanyowetsa minda yake komanso kusalaza dothi limene lalimidwa,*Mumaifewetsa ndi mvula yamvumbi. Mumadalitsa zomera zake.+