Salimo 66:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye akulamulira ndi mphamvu zake mpaka kalekale.+ Maso ake akuyangʼanitsitsa mitundu ya anthu.+ Anthu osamvera asadzikweze.+ (Selah)
7 Iye akulamulira ndi mphamvu zake mpaka kalekale.+ Maso ake akuyangʼanitsitsa mitundu ya anthu.+ Anthu osamvera asadzikweze.+ (Selah)