-
Salimo 66:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndidzapereka kwa inu nsembe zopsereza za nyama zonenepa,
Ndidzapereka nsembe nkhosa zamphongo.
Ndidzapereka ngʼombe zamphongo pamodzi ndi mbuzi zamphongo. (Selah)
-