Salimo 66:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati mumtima mwanga ndikanakhala ndi maganizo aliwonse oti ndichitire munthu zoipa,Yehova sakanandimvetsera.+
18 Ngati mumtima mwanga ndikanakhala ndi maganizo aliwonse oti ndichitire munthu zoipa,Yehova sakanandimvetsera.+