Salimo 66:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Mulungu anamva.+Anamvetsera pemphero langa mwatcheru.+