-
Salimo 66:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Atamandike Mulungu, amene sananyalanyaze pemphero langa
Kapena kulephera kundisonyeza chikondi chake chokhulupirika.
-