Salimo 68:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mofanana ndi mphepo imene imathamangitsa utsi, inunso muwathamangitsire kutali.Mofanana ndi phula limene limasungunuka pamoto,Anthu oipa awonongeke pamaso pa Mulungu.+
2 Mofanana ndi mphepo imene imathamangitsa utsi, inunso muwathamangitsire kutali.Mofanana ndi phula limene limasungunuka pamoto,Anthu oipa awonongeke pamaso pa Mulungu.+