Salimo 68:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma olungama asangalale,+Asangalale kwambiri pamaso pa Mulungu,Adumphe ndi chisangalalo.