Salimo 68:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Imbirani Mulungu, muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake.+ Imbirani Iye amene akudutsa mʼchipululu.* Dzina lake ndi Ya.*+ Sangalalani pamaso pake.
4 Imbirani Mulungu, muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake.+ Imbirani Iye amene akudutsa mʼchipululu.* Dzina lake ndi Ya.*+ Sangalalani pamaso pake.