Salimo 68:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Mulungu, munagwetsa mvula yokwanira.Munapatsa mphamvu anthu anu amene anali ofooka.*