Salimo 68:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo ankakhala mʼmudzi wanu wamatenti.+Inu Mulungu, chifukwa chakuti ndinu wabwino, munapereka zinthu zofunika kwa anthu osauka.
10 Iwo ankakhala mʼmudzi wanu wamatenti.+Inu Mulungu, chifukwa chakuti ndinu wabwino, munapereka zinthu zofunika kwa anthu osauka.