Salimo 68:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nʼchifukwa chiyani inu mapiri ansonga zitalizitali mumayangʼana mwansanjePhiri limene Mulungu wasankha* kuti azikhalamo?+ Ndithudi, Yehova adzakhala mʼphiri limenelo mpaka kalekale.+
16 Nʼchifukwa chiyani inu mapiri ansonga zitalizitali mumayangʼana mwansanjePhiri limene Mulungu wasankha* kuti azikhalamo?+ Ndithudi, Yehova adzakhala mʼphiri limenelo mpaka kalekale.+