Salimo 68:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo aona magulu a anthu anu akuyendera pamodzi, inu Mulungu,Magulu a anthu oyendera pamodzi a Mulungu wanga, Mfumu yanga, akulowa kumalo opatulika.+
24 Iwo aona magulu a anthu anu akuyendera pamodzi, inu Mulungu,Magulu a anthu oyendera pamodzi a Mulungu wanga, Mfumu yanga, akulowa kumalo opatulika.+