Salimo 68:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Oimba nyimbo akuyenda patsogolo, oimba zoimbira za zingwe akuyenda pambuyo pawo,+Pakati pali atsikana amene akuimba maseche.+
25 Oimba nyimbo akuyenda patsogolo, oimba zoimbira za zingwe akuyenda pambuyo pawo,+Pakati pali atsikana amene akuimba maseche.+