Salimo 68:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pali fuko lalingʼono la Benjamini+ limene likugonjetsa anthu,Pali akalonga a Yuda pamodzi ndi chigulu chawo chimene chikuchita phokoso,Palinso akalonga a Zebuloni komanso akalonga a Nafitali.
27 Pali fuko lalingʼono la Benjamini+ limene likugonjetsa anthu,Pali akalonga a Yuda pamodzi ndi chigulu chawo chimene chikuchita phokoso,Palinso akalonga a Zebuloni komanso akalonga a Nafitali.