Salimo 68:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mulungu wanu waganiza kuti akupatseni mphamvu. Sonyezani mphamvu zanu, Inu Mulungu, amene mumatithandiza.+
28 Mulungu wanu waganiza kuti akupatseni mphamvu. Sonyezani mphamvu zanu, Inu Mulungu, amene mumatithandiza.+