Salimo 68:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Imbirani iye amene wakwera pamwamba pa kumwamba,+ kumene kwakhalapo kuyambira kalekale. Mawu ake amphamvu amamveka ngati bingu.
33 Imbirani iye amene wakwera pamwamba pa kumwamba,+ kumene kwakhalapo kuyambira kalekale. Mawu ake amphamvu amamveka ngati bingu.