Salimo 68:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mulungu walamula kuti anthu amuope komanso amupatse ulemu mʼmalo ake opatulika aulemerero.+ Iye ndi Mulungu wa Isiraeli,Amene amapereka mphamvu ndi nyonga kwa anthu.+ Mulungu atamandike.
35 Mulungu walamula kuti anthu amuope komanso amupatse ulemu mʼmalo ake opatulika aulemerero.+ Iye ndi Mulungu wa Isiraeli,Amene amapereka mphamvu ndi nyonga kwa anthu.+ Mulungu atamandike.