Salimo 69:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipulumutseni mʼmatopeMusalole kuti ndimire. Ndipulumutseni kwa anthu amene amadana naneNdiponso ku madzi akuya.+
14 Ndipulumutseni mʼmatopeMusalole kuti ndimire. Ndipulumutseni kwa anthu amene amadana naneNdiponso ku madzi akuya.+