Salimo 69:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Musalole kuti madzi osefukira andikokolole,+Kapena kuti ndimire mʼmadzi akuya,Kapenanso kuti dzenje* lindimeze nʼkutseka pakamwa pake.+
15 Musalole kuti madzi osefukira andikokolole,+Kapena kuti ndimire mʼmadzi akuya,Kapenanso kuti dzenje* lindimeze nʼkutseka pakamwa pake.+