Salimo 69:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mtima wanga wasweka chifukwa cha kunyozedwa, ndipo bala lake ndi losachiritsika.* Ndimayembekezera kuti wina andimvera chisoni, koma panalibe ndi mmodzi yemwe,+Ndimayembekezera kuti wina anditonthoza, koma sanapezeke ngakhale mmodzi.+
20 Mtima wanga wasweka chifukwa cha kunyozedwa, ndipo bala lake ndi losachiritsika.* Ndimayembekezera kuti wina andimvera chisoni, koma panalibe ndi mmodzi yemwe,+Ndimayembekezera kuti wina anditonthoza, koma sanapezeke ngakhale mmodzi.+