Salimo 69:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tebulo lawo likhale msampha kwa iwo,Ndipo zinthu zimene zikuwayendera bwino zikhale ngati khwekhwe kwa iwo.+
22 Tebulo lawo likhale msampha kwa iwo,Ndipo zinthu zimene zikuwayendera bwino zikhale ngati khwekhwe kwa iwo.+