Salimo 69:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Zimenezi zidzasangalatsa kwambiri Yehova kuposa ngʼombe yamphongo,Kuposa ngʼombe yamphongo yaingʼono imene ili ndi nyanga komanso ziboda.+
31 Zimenezi zidzasangalatsa kwambiri Yehova kuposa ngʼombe yamphongo,Kuposa ngʼombe yamphongo yaingʼono imene ili ndi nyanga komanso ziboda.+