-
Salimo 70:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Amene amasangalala ndi njira imene mumapulumutsira anthu, nthawi zonse azinena kuti:
“Mulungu alemekezeke.”
-
Amene amasangalala ndi njira imene mumapulumutsira anthu, nthawi zonse azinena kuti:
“Mulungu alemekezeke.”