Salimo 71:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mukhale thanthwe langa lachitetezoLoti ndizilowamo nthawi zonse. Lamulani kuti ndipulumutsidwe,Chifukwa inu ndinu thanthwe langa ndi malo anga achitetezo.+
3 Mukhale thanthwe langa lachitetezoLoti ndizilowamo nthawi zonse. Lamulani kuti ndipulumutsidwe,Chifukwa inu ndinu thanthwe langa ndi malo anga achitetezo.+