Salimo 71:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa chiyembekezo changa ndi inu Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.Ndakhala ndikudalira inu kuyambira ndili mnyamata.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 71:5 Nsanja ya Olonda,9/1/1999, tsa. 18 Galamukani!,12/8/1995, tsa. 13
5 Chifukwa chiyembekezo changa ndi inu Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.Ndakhala ndikudalira inu kuyambira ndili mnyamata.+