Salimo 71:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Mulungu, musakhale kutali ndi ine. Inu Mulungu wanga, ndithandizeni mofulumira.+