-
Salimo 71:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndidzabwera nʼkudzanena za zinthu zamphamvu zimene mumachita,
Inu Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
Ndidzanena za chilungamo chanu chokha basi.
-