Salimo 71:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngakhale nditakalamba nʼkumera imvi, inu Mulungu musandisiye.+ Ndiloleni kuti ndiuze mʼbadwo wotsatira za mphamvu zanu*Komanso za nyonga zanu kwa onse obwera mʼtsogolo.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 71:18 Nsanja ya Olonda,1/15/2014, tsa. 236/1/2007, ptsa. 29-305/15/1997, ptsa. 19-20
18 Ngakhale nditakalamba nʼkumera imvi, inu Mulungu musandisiye.+ Ndiloleni kuti ndiuze mʼbadwo wotsatira za mphamvu zanu*Komanso za nyonga zanu kwa onse obwera mʼtsogolo.+