Salimo 71:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mukatero, ndidzakutamandani ndi choimbira cha zingweChifukwa cha kukhulupirika kwanu, inu Mulungu.+ Ndidzakuimbirani nyimbo zokutamandani ndi zeze,Inu Woyera wa Isiraeli.
22 Mukatero, ndidzakutamandani ndi choimbira cha zingweChifukwa cha kukhulupirika kwanu, inu Mulungu.+ Ndidzakuimbirani nyimbo zokutamandani ndi zeze,Inu Woyera wa Isiraeli.