Salimo 71:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakamwa panga padzafuula mosangalala pamene ndikuimba nyimbo zokutamandani,+Chifukwa mwapulumutsa moyo wanga.*+
23 Pakamwa panga padzafuula mosangalala pamene ndikuimba nyimbo zokutamandani,+Chifukwa mwapulumutsa moyo wanga.*+