Salimo 72:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ateteze* anthu onyozeka pakati pa anthu,Apulumutse ana a anthu osauka,Ndipo aphwanye wobera anzake mwachinyengo.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 72:4 Nsanja ya Olonda,8/15/2010, ptsa. 29-30
4 Ateteze* anthu onyozeka pakati pa anthu,Apulumutse ana a anthu osauka,Ndipo aphwanye wobera anzake mwachinyengo.+