Salimo 72:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzakhala ngati mvula imene imagwera pa udzu umene watchetchedwa,Ngati mvula yamvumbi imene imanyowetsa nthaka.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 72:6 Nsanja ya Olonda,8/15/2010, tsa. 30
6 Adzakhala ngati mvula imene imagwera pa udzu umene watchetchedwa,Ngati mvula yamvumbi imene imanyowetsa nthaka.+