Salimo 72:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzakhala ndi anthu omugonjera* kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,Komanso kuchokera ku Mtsinje* kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 72:8 Nsanja ya Olonda,8/15/2010, tsa. 31
8 Iye adzakhala ndi anthu omugonjera* kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,Komanso kuchokera ku Mtsinje* kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+