Salimo 72:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Adzawapulumutsa* kuti asaponderezedwe komanso kuchitiridwa zachiwawa,Ndipo adzaona kuti magazi awo ndi amtengo wapatali.
14 Adzawapulumutsa* kuti asaponderezedwe komanso kuchitiridwa zachiwawa,Ndipo adzaona kuti magazi awo ndi amtengo wapatali.