Salimo 72:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye akhale ndi moyo wautali ndipo apatsidwe golide wa ku Sheba.+ Nthawi zonse anthu azimupempherera,Ndipo azimudalitsa tsiku lililonse.
15 Iye akhale ndi moyo wautali ndipo apatsidwe golide wa ku Sheba.+ Nthawi zonse anthu azimupempherera,Ndipo azimudalitsa tsiku lililonse.