Salimo 72:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale,+Ndipo lipitirize kutchuka kwa nthawi zonse pamene dzuwa lidzakhalepo. Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.+Mitundu yonse ya anthu imutchule kuti ndi wosangalala. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 72:17 Nsanja ya Olonda,8/15/2010, tsa. 32
17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale,+Ndipo lipitirize kutchuka kwa nthawi zonse pamene dzuwa lidzakhalepo. Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.+Mitundu yonse ya anthu imutchule kuti ndi wosangalala.