Salimo 72:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Atamandike Yehova Mulungu, Mulungu wa Isiraeli,+Iye yekha amene amachita zinthu zodabwitsa.+