Salimo 73:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Winanso ndi ndani kumwambako amene angandithandize? Ndipo chifukwa chakuti inu muli ndi ine, palibenso chimene ndimalakalaka padziko lapansi.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 73:25 Nsanja ya Olonda,7/15/1993, ptsa. 30-31
25 Winanso ndi ndani kumwambako amene angandithandize? Ndipo chifukwa chakuti inu muli ndi ine, palibenso chimene ndimalakalaka padziko lapansi.+