Salimo 73:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndithudi, anthu amene ali kutali ndi inu adzatheratu. Mudzawononga* aliyense amene akukusiyani pochita chigololo.*+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 73:27 Nsanja ya Olonda,7/15/1993, ptsa. 30-31
27 Ndithudi, anthu amene ali kutali ndi inu adzatheratu. Mudzawononga* aliyense amene akukusiyani pochita chigololo.*+