Salimo 73:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma kwa ine, kuyandikira kwa Mulungu ndi chinthu chabwino.+ Ndapanga Yehova Ambuye Wamkulu Koposa kukhala malo anga othawirako,Kuti ndilengeze za ntchito zanu zonse.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 73:28 Nsanja ya Olonda,5/15/1997, tsa. 327/15/1993, ptsa. 30-31
28 Koma kwa ine, kuyandikira kwa Mulungu ndi chinthu chabwino.+ Ndapanga Yehova Ambuye Wamkulu Koposa kukhala malo anga othawirako,Kuti ndilengeze za ntchito zanu zonse.+