Salimo 74:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anagumula zinthu zojambula mochita kugoba zamʼmakoma a malo opatulika+ ndi nkhwangwa komanso ndodo zachitsulo.
6 Anagumula zinthu zojambula mochita kugoba zamʼmakoma a malo opatulika+ ndi nkhwangwa komanso ndodo zachitsulo.