Salimo 74:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anawotcha malo anu opatulika.+ Anaipitsa chihema chokhala ndi dzina lanu nʼkuchigwetsera pansi.