Salimo 74:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu Mulungu, kodi mdani adzapitiriza kunyoza mpaka liti?+ Kodi mdani adzachitira mwano dzina lanu mpaka kalekale?+
10 Inu Mulungu, kodi mdani adzapitiriza kunyoza mpaka liti?+ Kodi mdani adzachitira mwano dzina lanu mpaka kalekale?+