Salimo 74:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nʼchifukwa chiyani mwabweza dzanja lanu, dzanja lanu lamanja?+ Lichotseni pachifuwa panu ndipo muwawononge.
11 Nʼchifukwa chiyani mwabweza dzanja lanu, dzanja lanu lamanja?+ Lichotseni pachifuwa panu ndipo muwawononge.