Salimo 74:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nyamukani inu Mulungu, ndipo mudziteteze pa mlandu wanu. Kumbukirani mmene munthu wopusa wakunyozerani tsiku lonse.+
22 Nyamukani inu Mulungu, ndipo mudziteteze pa mlandu wanu. Kumbukirani mmene munthu wopusa wakunyozerani tsiku lonse.+