Salimo 75:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 75 Timakuyamikani, inu Mulungu, timakuyamikani.Dzina lanu lili pafupi ndi ife,+Ndipo anthu akulengeza ntchito zanu zodabwitsa.
75 Timakuyamikani, inu Mulungu, timakuyamikani.Dzina lanu lili pafupi ndi ife,+Ndipo anthu akulengeza ntchito zanu zodabwitsa.