Salimo 75:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu odzitukumula ndinawauza kuti, “Musadzitukumule,” Ndipo oipa ndinawauza kuti, “Musadzikuze chifukwa choti muli ndi mphamvu.*
4 Anthu odzitukumula ndinawauza kuti, “Musadzitukumule,” Ndipo oipa ndinawauza kuti, “Musadzikuze chifukwa choti muli ndi mphamvu.*