Salimo 75:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu akuti: “Ndidzathetsa mphamvu* zonse za anthu oipa,Koma ndidzachititsa kuti mphamvu* za anthu olungama zionekere bwino.” Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 75:10 Nsanja ya Olonda,7/15/2006, tsa. 1112/15/1986, tsa. 28
10 Mulungu akuti: “Ndidzathetsa mphamvu* zonse za anthu oipa,Koma ndidzachititsa kuti mphamvu* za anthu olungama zionekere bwino.”