Salimo 76:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kumeneko anathyola mivi yoyaka moto,Anathyolanso chishango, lupanga ndi zida zankhondo.+ (Selah)